Creation Science Information & Links!
Chikhulupiriro cha Atumwi
The Apostles' Creed - in Nyanja, Chichewa, Chinyanja

 

Ine ndikhulupirira Mulungu Atate wamphamvu-zonse,
Wolenga zakumwamba ndi za pansi pano.

Ndikhulupiriranso Yesu Kristu, mwana wake yekha, Ambuye athu,
Amene anapatsidwa ndi Mzimu Woyera,
Nabadwa mwa Maria namwaliyo,
Nazunzidwa kwa Pantiyo Pilato,
Napachikidwa pamtanda,
Namwalira, naikidwa m'manda,
Natsikira ku Gehena.
Mkucha wake Iye anauka kwa akufa.
Anakwera kumwamba,
Nakhala kudzanja lamanja la Mulungu Atate wamphamvu-zonse.
Kuchokera komweko adzabweranso kudzaweruza anthu amoyo ndi akufa.

Ndikhulupiriranso Mzimu Woyera,
Mpingo Woyera waChikristu,
Chiyanjano cha okhulupirira onse,
Chikhululukiro cha machimo,
Kuukanso kwa thupi,
Ndi moyo wosatha.
Ameni.


Chikhulupiriro cha Atumwi
http://www.creationism.org/chewa/saApostlesCreed_ny.htm

All Languages:  http://www.creationism.org/english/ApostlesCreed_Intl.htmSymbolum Apostolorum (Apostolicum)
  • 
Το Σύμβολο της Πίστεως
  • 
Basic Christian Theology (The Creed)

Main:  Nyanja
www.creationism.org